ZOMWE ZACHITIKA ATANGOFIKA PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA KU CONVENTION POMPANO

35,019
0
Published 2024-08-08

All Comments (21)
  • Chikangawa chakuba umu uzekuti machende ake achakwera yo onze makape dziko waliono nga agaluinu
  • @Eric-gb9ms
    Koma malo amenewa ali bho sangakwanise kumanga zake ulemu wanu Bingu
  • @KestonNGUBO
    Mafuta amen ayendera ni achipani kapen misonko yathu
  • Please where z chilima 😢😢😢😢😢😢😢😢 APM my vote DPP
  • Koma ku malawi wumphawi suzatha timangotengeka chifukwa cha ndarama
  • Nzofunia apange dzija wayankhula mbusa uja wakumwela dzokudya ndowe dzija kuti machimo ake akhululukidwe akalowe kumwamba ngati x mbusa wa Assembless coz apanga dzambiri
  • @chrisboyce2
    2025 nyau Out! tikufuna APM 💙 wachitukuko ife kuno ku Ntcheu osati Vigure aiii
  • Zaziii president ozikoma ngati uyo chifukwa choti pano walemera ndi misonkho ya Malawi nanga anali ndi chani akulowa muboma, azawo ana lamamphosa siozikonda chifukwa akulowa mu boma anali kali ndndlma ma business akulukulu azungunso akudziwa izi amampatsa ulemu koma uyo chikangawa kungopha anthu basi 😮😮😮😮😮
  • Zodedelykira chonchizi kawirikawiri timakonda kuzichita ndife amphawi pofunako ndalama chifukwa wina aliyese akudziwa bwino zammene zinthu ziliri Malawi ndiye palibe chifukwa chomataira nthawi nkumaimva akuti kulandira a president
  • Anthu amene akuchemelera chipan ichi iyeyo ndi mfiti bs chipan chakupha manja mwa chikangawa mwazaza magazi agalu inu
  • Mzimu wa Chilima ukukantheni munapha munthu wosalakwa anthu oyipa inu komaso ma siren ndi achani
  • Ufe sitimaonela za chikangawa party iyaaa athu akupha ngati awa afiti
  • Pali zanzeru zatumizidwapo apa kod aaaaa muziona zotumiza kapena mukufuna ma comments